×

Kotero Mulungu adzawalipira chifukwa cha ntchito zawo zabwino ndiponso adzawapatsa zabwino zochokera 24:38 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nur ⮕ (24:38) ayat 38 in Chichewa

24:38 Surah An-Nur ayat 38 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nur ayat 38 - النور - Page - Juz 18

﴿لِيَجۡزِيَهُمُ ٱللَّهُ أَحۡسَنَ مَا عَمِلُواْ وَيَزِيدَهُم مِّن فَضۡلِهِۦۗ وَٱللَّهُ يَرۡزُقُ مَن يَشَآءُ بِغَيۡرِ حِسَابٖ ﴾
[النور: 38]

Kotero Mulungu adzawalipira chifukwa cha ntchito zawo zabwino ndiponso adzawapatsa zabwino zochokera m’chisomo chake. Mulungu amapereka mopanda muyeso kwa aliyense amene Iye wamufuna

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ليجزيهم الله أحسن ما عملوا ويزيدهم من فضله والله يرزق من يشاء, باللغة نيانجا

﴿ليجزيهم الله أحسن ما عملوا ويزيدهم من فضله والله يرزق من يشاء﴾ [النور: 38]

Khaled Ibrahim Betala
“Kuti Allah adzawalipire zabwino pa zomwe adachita ndi kuwaonjezera zabwino Zake. Ndipo Allah amampatsa amene wamfuna popanda chiwerengero
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek