×

Iwo amalumbira pali Mulungu molimba kuti ngati iwe uwalamulira kumenya nkhondo, adzakumvera 24:53 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nur ⮕ (24:53) ayat 53 in Chichewa

24:53 Surah An-Nur ayat 53 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nur ayat 53 - النور - Page - Juz 18

﴿۞ وَأَقۡسَمُواْ بِٱللَّهِ جَهۡدَ أَيۡمَٰنِهِمۡ لَئِنۡ أَمَرۡتَهُمۡ لَيَخۡرُجُنَّۖ قُل لَّا تُقۡسِمُواْۖ طَاعَةٞ مَّعۡرُوفَةٌۚ إِنَّ ٱللَّهَ خَبِيرُۢ بِمَا تَعۡمَلُونَ ﴾
[النور: 53]

Iwo amalumbira pali Mulungu molimba kuti ngati iwe uwalamulira kumenya nkhondo, adzakumvera iwe. Nena “Musalumbire ayi! Chofunika ndi kumvera basi. Ndithudi Mulungu amadziwa chilichonse chimene mumachita.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وأقسموا بالله جهد أيمانهم لئن أمرتهم ليخرجن قل لا تقسموا طاعة معروفة, باللغة نيانجا

﴿وأقسموا بالله جهد أيمانهم لئن أمرتهم ليخرجن قل لا تقسموا طاعة معروفة﴾ [النور: 53]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo akulumbilira dzina la Allah, kulumbira kwakukulu kuti ukawalamula (kupita ku nkhondo), ndithu apita. Nena: “Musalumbire; kumvera kwanu nkodziwika (kuti nkwabodza); ndithu Allah akudziwa nkhani zonse zomwe muchita
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek