×

Nena, “Kodi chimenecho ndi chabwino kapena Paradiso yosatha imene anthu angwiro adalonjezedwa?” 25:15 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Furqan ⮕ (25:15) ayat 15 in Chichewa

25:15 Surah Al-Furqan ayat 15 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Furqan ayat 15 - الفُرقَان - Page - Juz 18

﴿قُلۡ أَذَٰلِكَ خَيۡرٌ أَمۡ جَنَّةُ ٱلۡخُلۡدِ ٱلَّتِي وُعِدَ ٱلۡمُتَّقُونَۚ كَانَتۡ لَهُمۡ جَزَآءٗ وَمَصِيرٗا ﴾
[الفُرقَان: 15]

Nena, “Kodi chimenecho ndi chabwino kapena Paradiso yosatha imene anthu angwiro adalonjezedwa?” Imeneyo ndiyo mphotho yawo ndi kobwerera kwawo

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قل أذلك خير أم جنة الخلد التي وعد المتقون كانت لهم جزاء, باللغة نيانجا

﴿قل أذلك خير أم جنة الخلد التي وعد المتقون كانت لهم جزاء﴾ [الفُرقَان: 15]

Khaled Ibrahim Betala
“Nena (kwa osakhulupirira): “Kodi izi ndizo zabwino, kapena munda wamuyaya umene alonjezedwa oopa Allah kuti udzakhale mphoto (yabwino) kwa iwo ndi kobwerera (kotamandika)?”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek