Quran with Chichewa translation - Surah Al-Furqan ayat 14 - الفُرقَان - Page - Juz 18
﴿لَّا تَدۡعُواْ ٱلۡيَوۡمَ ثُبُورٗا وَٰحِدٗا وَٱدۡعُواْ ثُبُورٗا كَثِيرٗا ﴾
[الفُرقَان: 14]
﴿لا تدعوا اليوم ثبورا واحدا وادعوا ثبورا كثيرا﴾ [الفُرقَان: 14]
Khaled Ibrahim Betala “(Tidzawauza): “Lero musaitane imfa imodzi, koma itanani imfa zambiri (ndipo simupeza mpumulo koma mazunzo okhaokha).” |