×

Nena “Ambuye wanga amakusamalani inu chifukwa cha mapempheroanuakwa Iyeyekha. Komatsopano, ndithudi, inu 25:77 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Furqan ⮕ (25:77) ayat 77 in Chichewa

25:77 Surah Al-Furqan ayat 77 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Furqan ayat 77 - الفُرقَان - Page - Juz 19

﴿قُلۡ مَا يَعۡبَؤُاْ بِكُمۡ رَبِّي لَوۡلَا دُعَآؤُكُمۡۖ فَقَدۡ كَذَّبۡتُمۡ فَسَوۡفَ يَكُونُ لِزَامَۢا ﴾
[الفُرقَان: 77]

Nena “Ambuye wanga amakusamalani inu chifukwa cha mapempheroanuakwa Iyeyekha. Komatsopano, ndithudi, inu mwamukana Iye. Motero chilango chidzakhala chanu mpaka kalekale.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قل ما يعبأ بكم ربي لولا دعاؤكم فقد كذبتم فسوف يكون لزاما, باللغة نيانجا

﴿قل ما يعبأ بكم ربي لولا دعاؤكم فقد كذبتم فسوف يكون لزاما﴾ [الفُرقَان: 77]

Khaled Ibrahim Betala
“Nena: “Ndithu Mbuye wanga sakadalabadira chilichonse pa inu pakadapanda mapemphero anu, (akadakulangani pompano pa dziko lapansi.) Komabe inu mwatsutsa (uthenga wa aneneri). Choncho chilango chidzakugweranibe.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek