Quran with Chichewa translation - Surah Ash-Shu‘ara’ ayat 30 - الشعراء - Page - Juz 19
﴿قَالَ أَوَلَوۡ جِئۡتُكَ بِشَيۡءٖ مُّبِينٖ ﴾
[الشعراء: 30]
﴿قال أو لو جئتك بشيء مبين﴾ [الشعراء: 30]
Khaled Ibrahim Betala “(Mûsa) adati: “Kodi ngakhale nditakubweretsera chinthu choonekera poyera (chosonyeza kuti zimene ndikunenazi ndizoona ndatumidwa ndi Allah)?” |