Quran with Chichewa translation - Surah An-Naml ayat 36 - النَّمل - Page - Juz 19
﴿فَلَمَّا جَآءَ سُلَيۡمَٰنَ قَالَ أَتُمِدُّونَنِ بِمَالٖ فَمَآ ءَاتَىٰنِۦَ ٱللَّهُ خَيۡرٞ مِّمَّآ ءَاتَىٰكُمۚ بَلۡ أَنتُم بِهَدِيَّتِكُمۡ تَفۡرَحُونَ ﴾
[النَّمل: 36]
﴿فلما جاء سليمان قال أتمدونن بمال فما آتاني الله خير مما آتاكم﴾ [النَّمل: 36]
Khaled Ibrahim Betala “Choncho pamene adafika (wamthenga wamkulu) kwa Sulaiman (ndi kupereka mphatso zija, Sulaiman adazikana) nati: “Mukundithandiza ndi chuma? zimene Allah wandipatsa ndizabwino kuposa zimene wakupatsani. Koma inu mukusangalala ndi mphatso zanu.” |