Quran with Chichewa translation - Surah An-Naml ayat 66 - النَّمل - Page - Juz 20
﴿بَلِ ٱدَّٰرَكَ عِلۡمُهُمۡ فِي ٱلۡأٓخِرَةِۚ بَلۡ هُمۡ فِي شَكّٖ مِّنۡهَاۖ بَلۡ هُم مِّنۡهَا عَمُونَ ﴾
[النَّمل: 66]
﴿بل ادارك علمهم في الآخرة بل هم في شك منها بل هم﴾ [النَّمل: 66]
Khaled Ibrahim Betala “Kwakhwima liti kudziwa kwawo (za kudza) kwa tsiku la chimaliziro? Koma iwo ali mchikaiko ndi za tsikulo; koma iwo ngakhungu pa zatsikulo |