Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qasas ayat 21 - القَصَص - Page - Juz 20
﴿فَخَرَجَ مِنۡهَا خَآئِفٗا يَتَرَقَّبُۖ قَالَ رَبِّ نَجِّنِي مِنَ ٱلۡقَوۡمِ ٱلظَّٰلِمِينَ ﴾
[القَصَص: 21]
﴿فخرج منها خائفا يترقب قال رب نجني من القوم الظالمين﴾ [القَصَص: 21]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo adachoka mu mzindawo ali woopa uku akuyembekezera (kumpeza choipa kuchokera kwa adani ake). Adati: “E Mbuye wanga! Ndipulumutseni kwa anthu ochita zoipa.” |