×

Koma Ife tidalenga mibadwo yambiri Mose atafa kale imene inali ndi moyo 28:45 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Qasas ⮕ (28:45) ayat 45 in Chichewa

28:45 Surah Al-Qasas ayat 45 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qasas ayat 45 - القَصَص - Page - Juz 20

﴿وَلَٰكِنَّآ أَنشَأۡنَا قُرُونٗا فَتَطَاوَلَ عَلَيۡهِمُ ٱلۡعُمُرُۚ وَمَا كُنتَ ثَاوِيٗا فِيٓ أَهۡلِ مَدۡيَنَ تَتۡلُواْ عَلَيۡهِمۡ ءَايَٰتِنَا وَلَٰكِنَّا كُنَّا مُرۡسِلِينَ ﴾
[القَصَص: 45]

Koma Ife tidalenga mibadwo yambiri Mose atafa kale imene inali ndi moyo wautali. Iwe siunakhale pakati pa anthu a ku Midiyani ndi kumawalakatulira chivumbulutso chathu. Koma Ife ndi amene timatumiza Atumwi

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولكنا أنشأنا قرونا فتطاول عليهم العمر وما كنت ثاويا في أهل مدين, باللغة نيانجا

﴿ولكنا أنشأنا قرونا فتطاول عليهم العمر وما كنت ثاويا في أهل مدين﴾ [القَصَص: 45]

Khaled Ibrahim Betala
“Koma ife tidaumba mibadwo yambiri (pambuyo pa Mneneri Mûsa) kotero kuti zaka zidapitapo zambiri pakati pawo. Ndipo sudakhale nawo anthu a Madiyan ndi kumawawerengera Ayah (ndime) Zathu; koma Ife tidali kutuma (atumiki ndi kuwafotokozera zomwe zidachitika patsogolo ndi pambuyo pawo, monga momwe takutumira iwe ndi kukudziwitsa nkhani zakale ndi zimene zikudza pambuyo)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek