×

Ndipo iwe kudalibe m’mbali mwa phiri la Sinai pamene tidamuitana Mose. Koma 28:46 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Qasas ⮕ (28:46) ayat 46 in Chichewa

28:46 Surah Al-Qasas ayat 46 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qasas ayat 46 - القَصَص - Page - Juz 20

﴿وَمَا كُنتَ بِجَانِبِ ٱلطُّورِ إِذۡ نَادَيۡنَا وَلَٰكِن رَّحۡمَةٗ مِّن رَّبِّكَ لِتُنذِرَ قَوۡمٗا مَّآ أَتَىٰهُم مِّن نَّذِيرٖ مِّن قَبۡلِكَ لَعَلَّهُمۡ يَتَذَكَّرُونَ ﴾
[القَصَص: 46]

Ndipo iwe kudalibe m’mbali mwa phiri la Sinai pamene tidamuitana Mose. Koma adali madalitso ochokera kwa Ambuye wako kuti ukachenjeze mtundu wa anthu umene unalipo iwe usanadze kotero kuti akhoza kuchenjezedwa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وما كنت بجانب الطور إذ نادينا ولكن رحمة من ربك لتنذر قوما, باللغة نيانجا

﴿وما كنت بجانب الطور إذ نادينا ولكن رحمة من ربك لتنذر قوما﴾ [القَصَص: 46]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo sudali kumbali kwa phiri pamene tidamuitana (Mneneri Mûsa). Koma (kutumidwa kwako) ndimtendere wochokera kwa Mbuye wako kuti uwachenjeze anthu omwe mchenjezi sadawadzere (mnthawi yaitali) iwe usadadze, kuti akumbukire
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek