×

Tikanapanda kukutumiza iwe ndipo mazunzo akadawagwera chifukwa cha ntchito zawo zoipa, iwo 28:47 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Qasas ⮕ (28:47) ayat 47 in Chichewa

28:47 Surah Al-Qasas ayat 47 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qasas ayat 47 - القَصَص - Page - Juz 20

﴿وَلَوۡلَآ أَن تُصِيبَهُم مُّصِيبَةُۢ بِمَا قَدَّمَتۡ أَيۡدِيهِمۡ فَيَقُولُواْ رَبَّنَا لَوۡلَآ أَرۡسَلۡتَ إِلَيۡنَا رَسُولٗا فَنَتَّبِعَ ءَايَٰتِكَ وَنَكُونَ مِنَ ٱلۡمُؤۡمِنِينَ ﴾
[القَصَص: 47]

Tikanapanda kukutumiza iwe ndipo mazunzo akadawagwera chifukwa cha ntchito zawo zoipa, iwo akadati, “Ambuye, chifukwa chiyani simudatitumizire Mtumwi kotero kuti tikadatsatira mawu anu ndiponso tikadakhala okhulupirira.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولولا أن تصيبهم مصيبة بما قدمت أيديهم فيقولوا ربنا لولا أرسلت إلينا, باللغة نيانجا

﴿ولولا أن تصيبهم مصيبة بما قدمت أيديهم فيقولوا ربنا لولا أرسلت إلينا﴾ [القَصَص: 47]

Khaled Ibrahim Betala
“(Ndipo sitikadatuma) koma kuti mavuto akawapeza ochokera (ku zoipa) zomwe atsogoza manja awo, amanena: “Mbuye wathu! Bwanji wosatitumizira Mtumiki kuti titsate mawu anu ndi kukhala mwa okhulupirira.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek