Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qasas ayat 49 - القَصَص - Page - Juz 20
﴿قُلۡ فَأۡتُواْ بِكِتَٰبٖ مِّنۡ عِندِ ٱللَّهِ هُوَ أَهۡدَىٰ مِنۡهُمَآ أَتَّبِعۡهُ إِن كُنتُمۡ صَٰدِقِينَ ﴾
[القَصَص: 49]
﴿قل فأتوا بكتاب من عند الله هو أهدى منهما أتبعه إن كنتم﴾ [القَصَص: 49]
Khaled Ibrahim Betala “Nena: “Bwerani nalo buku lochokera kwa Allah lomwe lili ndi chiongoko chabwino kuposa awiriwa (Taurati ya Mneneri Mûsa, ndi iyi Qur’an), kuti ndilitsate ngati inu mukunena zoona.” |