×

Ndithudi Iye amene adalamulira Buku la Korani kuti livumbulutsidwe kwa iwe adzakubwezera 28:85 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Qasas ⮕ (28:85) ayat 85 in Chichewa

28:85 Surah Al-Qasas ayat 85 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qasas ayat 85 - القَصَص - Page - Juz 20

﴿إِنَّ ٱلَّذِي فَرَضَ عَلَيۡكَ ٱلۡقُرۡءَانَ لَرَآدُّكَ إِلَىٰ مَعَادٖۚ قُل رَّبِّيٓ أَعۡلَمُ مَن جَآءَ بِٱلۡهُدَىٰ وَمَنۡ هُوَ فِي ضَلَٰلٖ مُّبِينٖ ﴾
[القَصَص: 85]

Ndithudi Iye amene adalamulira Buku la Korani kuti livumbulutsidwe kwa iwe adzakubwezera kumalo komwe udzapite. Nena, “Ambuye wanga adziwa bwino iye amene amabweretsa langizo loonadi ndiponso iye amene ndi wosochera.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إن الذي فرض عليك القرآن لرادك إلى معاد قل ربي أعلم من, باللغة نيانجا

﴿إن الذي فرض عليك القرآن لرادك إلى معاد قل ربي أعلم من﴾ [القَصَص: 85]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithudi yemwe wakulamula kuitsata Qur’an, mwachoonadi adzakubwezera pa malo pobwerera. Nena! “Mbuye wanga ndi yemwe akudziwa amene wadza ndi chiongoko ndi yemwe ali m’kusokera koonekera poyera.’’
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek