Quran with Chichewa translation - Surah al-‘Imran ayat 158 - آل عِمران - Page - Juz 4
﴿وَلَئِن مُّتُّمۡ أَوۡ قُتِلۡتُمۡ لَإِلَى ٱللَّهِ تُحۡشَرُونَ ﴾
[آل عِمران: 158]
﴿ولئن متم أو قتلتم لإلى الله تحشرون﴾ [آل عِمران: 158]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo ngati mumwalira kapena kuphedwa (n’chimodzimodzi), ndithudi nonsenu mudzasonkhanitsidwa kwa Allah |