Quran with Chichewa translation - Surah al-‘Imran ayat 157 - آل عِمران - Page - Juz 4
﴿وَلَئِن قُتِلۡتُمۡ فِي سَبِيلِ ٱللَّهِ أَوۡ مُتُّمۡ لَمَغۡفِرَةٞ مِّنَ ٱللَّهِ وَرَحۡمَةٌ خَيۡرٞ مِّمَّا يَجۡمَعُونَ ﴾
[آل عِمران: 157]
﴿ولئن قتلتم في سبيل الله أو متم لمغفرة من الله ورحمة خير﴾ [آل عِمران: 157]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo ngati mwaphedwa pa njira ya Allah, kapena kufa, (palibe chotaika kwa inu) pakuti chikhululuko ndi chisoni zochokera kwa Allah nzabwino kuposa zomwe akuzisonkhanitsa (pa moyo wa pa dziko lapansi) |