Quran with Chichewa translation - Surah al-‘Imran ayat 25 - آل عِمران - Page - Juz 3
﴿فَكَيۡفَ إِذَا جَمَعۡنَٰهُمۡ لِيَوۡمٖ لَّا رَيۡبَ فِيهِ وَوُفِّيَتۡ كُلُّ نَفۡسٖ مَّا كَسَبَتۡ وَهُمۡ لَا يُظۡلَمُونَ ﴾ 
[آل عِمران: 25]
﴿فكيف إذا جمعناهم ليوم لا ريب فيه ووفيت كل نفس ما كسبت﴾ [آل عِمران: 25]
| Khaled Ibrahim Betala “Kodi zidzakhala zotani pamene tidzawasonkhanitsa tsiku lopanda chikaiko? Ndipo mzimu uliwonse udzalipidwa mokwanira pa zomwe udachita. Ndipo iwo sadzaponderezedwa |