×

Lapani kwa Iye ndiponso muopeni Iye. Pitirizani kupemphera nthawi zonse ndipo musakhale 30:31 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Ar-Rum ⮕ (30:31) ayat 31 in Chichewa

30:31 Surah Ar-Rum ayat 31 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Ar-Rum ayat 31 - الرُّوم - Page - Juz 21

﴿۞ مُنِيبِينَ إِلَيۡهِ وَٱتَّقُوهُ وَأَقِيمُواْ ٱلصَّلَوٰةَ وَلَا تَكُونُواْ مِنَ ٱلۡمُشۡرِكِينَ ﴾
[الرُّوم: 31]

Lapani kwa Iye ndiponso muopeni Iye. Pitirizani kupemphera nthawi zonse ndipo musakhale inu pakati pa iwo amene amafanizira milungu ina ndi Mulungu weniweni

❮ Previous Next ❯

ترجمة: منيبين إليه واتقوه وأقيموا الصلاة ولا تكونوا من المشركين, باللغة نيانجا

﴿منيبين إليه واتقوه وأقيموا الصلاة ولا تكونوا من المشركين﴾ [الرُّوم: 31]

Khaled Ibrahim Betala
“(Lunjikani nkhope zanu) modzichepetsa kwa Iye ndipo muopeni (potsatira malamulo Ake). Pempherani Swala moyenera, ndipo musakhale mwa opembedza mafano
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek