Quran with Chichewa translation - Surah As-Sajdah ayat 30 - السَّجدة - Page - Juz 21
﴿فَأَعۡرِضۡ عَنۡهُمۡ وَٱنتَظِرۡ إِنَّهُم مُّنتَظِرُونَ ﴾
[السَّجدة: 30]
﴿فأعرض عنهم وانتظر إنهم منتظرون﴾ [السَّجدة: 30]
Khaled Ibrahim Betala “Choncho apatuke; ndipo yembekezera (zimene Allah wakulonjeza). Ndithu nawonso akuyembekezera (zimene Allah wawalonjeza) |