×

Ndi njiru imene ali nayo pa iwe, pamene choopsa chidza, iwe udzawaona 33:19 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ahzab ⮕ (33:19) ayat 19 in Chichewa

33:19 Surah Al-Ahzab ayat 19 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ahzab ayat 19 - الأحزَاب - Page - Juz 21

﴿أَشِحَّةً عَلَيۡكُمۡۖ فَإِذَا جَآءَ ٱلۡخَوۡفُ رَأَيۡتَهُمۡ يَنظُرُونَ إِلَيۡكَ تَدُورُ أَعۡيُنُهُمۡ كَٱلَّذِي يُغۡشَىٰ عَلَيۡهِ مِنَ ٱلۡمَوۡتِۖ فَإِذَا ذَهَبَ ٱلۡخَوۡفُ سَلَقُوكُم بِأَلۡسِنَةٍ حِدَادٍ أَشِحَّةً عَلَى ٱلۡخَيۡرِۚ أُوْلَٰٓئِكَ لَمۡ يُؤۡمِنُواْ فَأَحۡبَطَ ٱللَّهُ أَعۡمَٰلَهُمۡۚ وَكَانَ ذَٰلِكَ عَلَى ٱللَّهِ يَسِيرٗا ﴾
[الأحزَاب: 19]

Ndi njiru imene ali nayo pa iwe, pamene choopsa chidza, iwe udzawaona ali kukuyang’ana, maso awo ali kutembenuzika, monga munthu amene ali pafupi kufa. Komangatichoopsachidutsaiwoamakunyozandimalirime awo akuthwa chifukwa cha njiru pa zinthu zabwino zimene uli nazo. Awa sadakhulupirire ndipo Mulungu wasandutsa zochita zawo kukhala zopanda pake ndipo zimenezi si zovuta kwa Mulungu

❮ Previous Next ❯

ترجمة: أشحة عليكم فإذا جاء الخوف رأيتهم ينظرون إليك تدور أعينهم كالذي يغشى, باللغة نيانجا

﴿أشحة عليكم فإذا جاء الخوف رأيتهم ينظرون إليك تدور أعينهم كالذي يغشى﴾ [الأحزَاب: 19]

Khaled Ibrahim Betala
“Okuchitirani inu umbombo (pa chikondi ndi pa chifundo; sakufunirani zabwino). Koma mantha akadza uwaona akukuyang’ana, uku maso awo akutembenuka (mophethiraphethira) monga a amene wakomoledwa ndi imfa. Koma mantha akachoka, akukupatsani masautso ndi malirime awo akuthwa; mbombo pa chabwino chilichonse. Iwowo sadakhulupirire ndipo choncho Allah wagwetsa malipiro a zochita zawo. Zimenezo nzosavuta kwa Allah
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek