Quran with Chichewa translation - Surah Saba’ ayat 51 - سَبإ - Page - Juz 22
﴿وَلَوۡ تَرَىٰٓ إِذۡ فَزِعُواْ فَلَا فَوۡتَ وَأُخِذُواْ مِن مَّكَانٖ قَرِيبٖ ﴾
[سَبإ: 51]
﴿ولو ترى إذ فزعوا فلا فوت وأخذوا من مكان قريب﴾ [سَبإ: 51]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo ukadaona pamene adzanjenjemera (akadzachiona chilango cha Allah, adzayesera kuthawa), koma sipadzapezeka pothawira, ndipo adzagwidwa pamtunda wapafupi (asanafike kutali) |