Quran with Chichewa translation - Surah Saba’ ayat 52 - سَبإ - Page - Juz 22
﴿وَقَالُوٓاْ ءَامَنَّا بِهِۦ وَأَنَّىٰ لَهُمُ ٱلتَّنَاوُشُ مِن مَّكَانِۭ بَعِيدٖ ﴾
[سَبإ: 52]
﴿وقالوا آمنا به وأنى لهم التناوش من مكان بعيد﴾ [سَبإ: 52]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo adzanena (mophuphaphupha): “Tachikhulupirira (tsopano chipembedzo cha Chisilamu).” Koma iwo angaulandire chotani (Usilamu) kumeneko (komwe) ndikumalo akutali |