Quran with Chichewa translation - Surah FaTir ayat 14 - فَاطِر - Page - Juz 22
﴿إِن تَدۡعُوهُمۡ لَا يَسۡمَعُواْ دُعَآءَكُمۡ وَلَوۡ سَمِعُواْ مَا ٱسۡتَجَابُواْ لَكُمۡۖ وَيَوۡمَ ٱلۡقِيَٰمَةِ يَكۡفُرُونَ بِشِرۡكِكُمۡۚ وَلَا يُنَبِّئُكَ مِثۡلُ خَبِيرٖ ﴾
[فَاطِر: 14]
﴿إن تدعوهم لا يسمعوا دعاءكم ولو سمعوا ما استجابوا لكم ويوم القيامة﴾ [فَاطِر: 14]
Khaled Ibrahim Betala “Ngati mutawapempha (mafanowo), sangamve kuitana kwanu, ndipo ngati atamva sangakuyankheni (chifukwa alibe kukhoza kulikonse). Ndipo pa tsiku lomalizira, adzakana kuphatikiza kwanu. Ndipo palibe (aliyense) angakuuze monga momwe akukuuzira (Allah) Wodziwa kwambiri |