×

Ndipo ngati akuti iwe ndi wabodza, ndithudi, Atumwi amene adadza iwe usanabadwe 35:4 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah FaTir ⮕ (35:4) ayat 4 in Chichewa

35:4 Surah FaTir ayat 4 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah FaTir ayat 4 - فَاطِر - Page - Juz 22

﴿وَإِن يُكَذِّبُوكَ فَقَدۡ كُذِّبَتۡ رُسُلٞ مِّن قَبۡلِكَۚ وَإِلَى ٱللَّهِ تُرۡجَعُ ٱلۡأُمُورُ ﴾
[فَاطِر: 4]

Ndipo ngati akuti iwe ndi wabodza, ndithudi, Atumwi amene adadza iwe usanabadwe nawonso adatchulidwa kuti ndi abodza ndipo ndi kwa Mulungu kokha kumene zinthu zonse zidzabwerera

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإن يكذبوك فقد كذبت رسل من قبلك وإلى الله ترجع الأمور, باللغة نيانجا

﴿وإن يكذبوك فقد كذبت رسل من قبلك وإلى الله ترجع الأمور﴾ [فَاطِر: 4]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo ngati angakutsutse ndithu adatsutsidwanso atumiki amene adalipo patsogolo pako. Ndipo zinthu zonse zidzabwezedwa kwa Allah
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek