×

Anthu inu! Ndithudi lonjezo la Mulungu ndi loona, kotero musalole zokoma za 35:5 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah FaTir ⮕ (35:5) ayat 5 in Chichewa

35:5 Surah FaTir ayat 5 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah FaTir ayat 5 - فَاطِر - Page - Juz 22

﴿يَٰٓأَيُّهَا ٱلنَّاسُ إِنَّ وَعۡدَ ٱللَّهِ حَقّٞۖ فَلَا تَغُرَّنَّكُمُ ٱلۡحَيَوٰةُ ٱلدُّنۡيَا وَلَا يَغُرَّنَّكُم بِٱللَّهِ ٱلۡغَرُورُ ﴾
[فَاطِر: 5]

Anthu inu! Ndithudi lonjezo la Mulungu ndi loona, kotero musalole zokoma za m’moyo uno kuti zikunyengeni ndiponso musalole mdyerekezi kuti akunyengeni zokhudza Mulungu

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ياأيها الناس إن وعد الله حق فلا تغرنكم الحياة الدنيا ولا يغرنكم, باللغة نيانجا

﴿ياأيها الناس إن وعد الله حق فلا تغرنكم الحياة الدنيا ولا يغرنكم﴾ [فَاطِر: 5]

Khaled Ibrahim Betala
“E inu anthu! Ndithu lonjezo la Allah ndi loona. Choncho usakunyengeni moyo wa dziko lapansi, ngakhale mdyerekezi uja wamkulu (Iblis), asakunyengeni pa za Allah
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek