×

Ndithudi ndi Mulungu amene amayang’anira kumwamba ndi dziko lapansi kuti zingaonongeke ndipo 35:41 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah FaTir ⮕ (35:41) ayat 41 in Chichewa

35:41 Surah FaTir ayat 41 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah FaTir ayat 41 - فَاطِر - Page - Juz 22

﴿۞ إِنَّ ٱللَّهَ يُمۡسِكُ ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَٱلۡأَرۡضَ أَن تَزُولَاۚ وَلَئِن زَالَتَآ إِنۡ أَمۡسَكَهُمَا مِنۡ أَحَدٖ مِّنۢ بَعۡدِهِۦٓۚ إِنَّهُۥ كَانَ حَلِيمًا غَفُورٗا ﴾
[فَاطِر: 41]

Ndithudi ndi Mulungu amene amayang’anira kumwamba ndi dziko lapansi kuti zingaonongeke ndipo izo zitaonongeka palibe wina amene akhoza kuzikonzanso kupatula Iye yekha. Ndithudi Iye ndi wopirira ndi wokhululukira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إن الله يمسك السموات والأرض أن تزولا ولئن زالتا إن أمسكهما من, باللغة نيانجا

﴿إن الله يمسك السموات والأرض أن تزولا ولئن زالتا إن أمسكهما من﴾ [فَاطِر: 41]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithu Allah amagwira thambo ndi nthaka kuti zisachoke. Ndipo ngati zitachoka, palibe aliyense amene angazigwire kupatula Iye. Ndithu Iye Ngoleza; Ngokhululuka kwabasi
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek