×

Ndipo iwo adalumbira motchula Mulungu ndi molimbika kuti ngati kungadze kwa iwo 35:42 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah FaTir ⮕ (35:42) ayat 42 in Chichewa

35:42 Surah FaTir ayat 42 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah FaTir ayat 42 - فَاطِر - Page - Juz 22

﴿وَأَقۡسَمُواْ بِٱللَّهِ جَهۡدَ أَيۡمَٰنِهِمۡ لَئِن جَآءَهُمۡ نَذِيرٞ لَّيَكُونُنَّ أَهۡدَىٰ مِنۡ إِحۡدَى ٱلۡأُمَمِۖ فَلَمَّا جَآءَهُمۡ نَذِيرٞ مَّا زَادَهُمۡ إِلَّا نُفُورًا ﴾
[فَاطِر: 42]

Ndipo iwo adalumbira motchula Mulungu ndi molimbika kuti ngati kungadze kwa iwo Mtumwi iwo adzalandira ulangizi wake kuposa mtundu wina uliwonse. Koma pamene Mtumwi adadza kwa iwo, kubwera kwake kudaonjezera kuipa kwawo

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وأقسموا بالله جهد أيمانهم لئن جاءهم نذير ليكونن أهدى من إحدى الأمم, باللغة نيانجا

﴿وأقسموا بالله جهد أيمانهم لئن جاءهم نذير ليكونن أهدى من إحدى الأمم﴾ [فَاطِر: 42]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo (awa osakhulupirira, kale) adalumbilira Allah, kulumbira kwawo kwakukulu, kuti ngati adzawadzera mchenjezi, adzakhala oongoka kuposa mbadwo uliwonse. Koma pamene mchenjezi adawadzera, palibe chilichonse chidaonjezeka kwa iwo, koma kukana (choonadicho)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek