×

Aliyense amene afuna ulemu ndi mphamvu ndi kwa Mulungu kumene kuli ulemu 35:10 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah FaTir ⮕ (35:10) ayat 10 in Chichewa

35:10 Surah FaTir ayat 10 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah FaTir ayat 10 - فَاطِر - Page - Juz 22

﴿مَن كَانَ يُرِيدُ ٱلۡعِزَّةَ فَلِلَّهِ ٱلۡعِزَّةُ جَمِيعًاۚ إِلَيۡهِ يَصۡعَدُ ٱلۡكَلِمُ ٱلطَّيِّبُ وَٱلۡعَمَلُ ٱلصَّٰلِحُ يَرۡفَعُهُۥۚ وَٱلَّذِينَ يَمۡكُرُونَ ٱلسَّيِّـَٔاتِ لَهُمۡ عَذَابٞ شَدِيدٞۖ وَمَكۡرُ أُوْلَٰٓئِكَ هُوَ يَبُورُ ﴾
[فَاطِر: 10]

Aliyense amene afuna ulemu ndi mphamvu ndi kwa Mulungu kumene kuli ulemu ndi mphamvu. Kwa Iye ndiko kumene kumapita mawu abwino ndipo ntchito zabwino amazinyamula. Akakhala iwo amene amakonza ntchito zoipa, iwo adzalandira chilango chowawa ndipo chikonzero chawo chidzafafanizidwa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: من كان يريد العزة فلله العزة جميعا إليه يصعد الكلم الطيب والعمل, باللغة نيانجا

﴿من كان يريد العزة فلله العزة جميعا إليه يصعد الكلم الطيب والعمل﴾ [فَاطِر: 10]

Khaled Ibrahim Betala
“Amene akufuna ulemelero, (amvere Allah), chifukwa ulemelero wonse ngwa Allah. Kwa Iye amakwera mawu abwino. Ndipo zochita zabwino ndi zimene zimakweza mawu abwinowo. Ndipo amene akuchita ndale zoipa, adzapeza chilango chaukali; ndipo ndale zawo nzoonongeka
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek