Quran with Chichewa translation - Surah Ya-Sin ayat 15 - يسٓ - Page - Juz 22
﴿قَالُواْ مَآ أَنتُمۡ إِلَّا بَشَرٞ مِّثۡلُنَا وَمَآ أَنزَلَ ٱلرَّحۡمَٰنُ مِن شَيۡءٍ إِنۡ أَنتُمۡ إِلَّا تَكۡذِبُونَ ﴾
[يسٓ: 15]
﴿قالوا ما أنتم إلا بشر مثلنا وما أنـزل الرحمن من شيء إن﴾ [يسٓ: 15]
Khaled Ibrahim Betala “(Eni mudzi) adati: “Inu ndi anthu ngati ife; (Allah) Wachifundo chambiri sadavumbulutse chilichonse (kwa munthu); inu simuli kanthu koma mukunena bodza.” |