×

Ulemerero ukhale kwa Iye amene adalenga zinthu ziwiriziwiri, (chachimuna ndi chachikazi) zimene 36:36 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Ya-Sin ⮕ (36:36) ayat 36 in Chichewa

36:36 Surah Ya-Sin ayat 36 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Ya-Sin ayat 36 - يسٓ - Page - Juz 23

﴿سُبۡحَٰنَ ٱلَّذِي خَلَقَ ٱلۡأَزۡوَٰجَ كُلَّهَا مِمَّا تُنۢبِتُ ٱلۡأَرۡضُ وَمِنۡ أَنفُسِهِمۡ وَمِمَّا لَا يَعۡلَمُونَ ﴾
[يسٓ: 36]

Ulemerero ukhale kwa Iye amene adalenga zinthu ziwiriziwiri, (chachimuna ndi chachikazi) zimene zimamera m’nthaka ndi zina za mtundu wawo ndi zinanso zimene sazidziwa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: سبحان الذي خلق الأزواج كلها مما تنبت الأرض ومن أنفسهم ومما لا, باللغة نيانجا

﴿سبحان الذي خلق الأزواج كلها مما تنبت الأرض ومن أنفسهم ومما لا﴾ [يسٓ: 36]

Khaled Ibrahim Betala
“Alemekezeke (Allah), Amene adalenga zinthu zonse, chachimuna ndi chachikazi, kuchokera m’zimene nthaka ikutulutsa, ndi iwo omwe ndi zina zimene (anthu) sakudziwa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek