Quran with Chichewa translation - Surah Ya-Sin ayat 37 - يسٓ - Page - Juz 23
﴿وَءَايَةٞ لَّهُمُ ٱلَّيۡلُ نَسۡلَخُ مِنۡهُ ٱلنَّهَارَ فَإِذَا هُم مُّظۡلِمُونَ ﴾
[يسٓ: 37]
﴿وآية لهم الليل نسلخ منه النهار فإذا هم مظلمون﴾ [يسٓ: 37]
Khaled Ibrahim Betala “Ndiponso chisonyezo chawo ndiusiku. M’menemo timachotsamo usana (womwe umabisa usiku), ndipo (anthu) amangozindikira ali mu mdima |