Quran with Chichewa translation - Surah Ya-Sin ayat 38 - يسٓ - Page - Juz 23
﴿وَٱلشَّمۡسُ تَجۡرِي لِمُسۡتَقَرّٖ لَّهَاۚ ذَٰلِكَ تَقۡدِيرُ ٱلۡعَزِيزِ ٱلۡعَلِيمِ ﴾
[يسٓ: 38]
﴿والشمس تجري لمستقر لها ذلك تقدير العزيز العليم﴾ [يسٓ: 38]
Khaled Ibrahim Betala “۞ Ndipo dzuwa; limayenda m’njira ndi m’nthawi yake imene idakonzedwa kwa ilo. Chikonzero chimenecho ncha (Allah) Wamphamvu zoposa, Wodziwa kwambiri |