Quran with Chichewa translation - Surah Ya-Sin ayat 39 - يسٓ - Page - Juz 23
﴿وَٱلۡقَمَرَ قَدَّرۡنَٰهُ مَنَازِلَ حَتَّىٰ عَادَ كَٱلۡعُرۡجُونِ ٱلۡقَدِيمِ ﴾
[يسٓ: 39]
﴿والقمر قدرناه منازل حتى عاد كالعرجون القديم﴾ [يسٓ: 39]
Khaled Ibrahim Betala “Ndiponso mwezi; tidaukonzera malo oimirapo mpaka kukafika pomwe umabwerera ndi kukhala wochepa ndi wokhota monga nthambi ya mtengo wa kanjedza, youma komanso yokhota |