Quran with Chichewa translation - Surah Ya-Sin ayat 78 - يسٓ - Page - Juz 23
﴿وَضَرَبَ لَنَا مَثَلٗا وَنَسِيَ خَلۡقَهُۥۖ قَالَ مَن يُحۡيِ ٱلۡعِظَٰمَ وَهِيَ رَمِيمٞ ﴾
[يسٓ: 78]
﴿وضرب لنا مثلا ونسي خلقه قال من يحيي العظام وهي رميم﴾ [يسٓ: 78]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo akutiponyera fanizo (lotsutsa kukhoza Kwathu kuukitsa akufa) ndi kuiwala chilengedwe chake (chochokera kumadzi opanda pake). Akunena: “Ndani angaukitse mafupa pomwe ali ofumbwa?” |