Quran with Chichewa translation - Surah As-saffat ayat 28 - الصَّافَات - Page - Juz 23
﴿قَالُوٓاْ إِنَّكُمۡ كُنتُمۡ تَأۡتُونَنَا عَنِ ٱلۡيَمِينِ ﴾
[الصَّافَات: 28]
﴿قالوا إنكم كنتم تأتوننا عن اليمين﴾ [الصَّافَات: 28]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo (ofooka) adzanena (kwa odzikweza): “Inu mumatidzera kumbali komwe timakuganizira kuti nkwabwino (ndi kutichotsako kunka nafe ku njira yopotoka) |