×

Kotero iwo sangathe kumvetsera zokambidwa za gulu lapamwamba chifukwa iwo amapirikitsidwa kuchokera 37:8 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah As-saffat ⮕ (37:8) ayat 8 in Chichewa

37:8 Surah As-saffat ayat 8 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah As-saffat ayat 8 - الصَّافَات - Page - Juz 23

﴿لَّا يَسَّمَّعُونَ إِلَى ٱلۡمَلَإِ ٱلۡأَعۡلَىٰ وَيُقۡذَفُونَ مِن كُلِّ جَانِبٖ ﴾
[الصَّافَات: 8]

Kotero iwo sangathe kumvetsera zokambidwa za gulu lapamwamba chifukwa iwo amapirikitsidwa kuchokera kumbali iliyonse

❮ Previous Next ❯

ترجمة: لا يسمعون إلى الملإ الأعلى ويقذفون من كل جانب, باللغة نيانجا

﴿لا يسمعون إلى الملإ الأعلى ويقذفون من كل جانب﴾ [الصَّافَات: 8]

Khaled Ibrahim Betala
“Kuti asamvere (zomwe zikunenedwa ndi) gulu lolemekezeka (la angelo). Ndipo akugendedwa (ndi kupirikitsidwa) mbali zonse
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek