×

Kodi Mulungu sakwana kuthandiza akapolo ake? Komabe iwo amayesetsa kukuopseza ndi milungu 39:36 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Az-Zumar ⮕ (39:36) ayat 36 in Chichewa

39:36 Surah Az-Zumar ayat 36 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zumar ayat 36 - الزُّمَر - Page - Juz 24

﴿أَلَيۡسَ ٱللَّهُ بِكَافٍ عَبۡدَهُۥۖ وَيُخَوِّفُونَكَ بِٱلَّذِينَ مِن دُونِهِۦۚ وَمَن يُضۡلِلِ ٱللَّهُ فَمَا لَهُۥ مِنۡ هَادٖ ﴾
[الزُّمَر: 36]

Kodi Mulungu sakwana kuthandiza akapolo ake? Komabe iwo amayesetsa kukuopseza ndi milungu ina yoonjezera pa Iye. Ndipo aliyense amene Mulungu amusocheza alibe wina womutsogolera

❮ Previous Next ❯

ترجمة: أليس الله بكاف عبده ويخوفونك بالذين من دونه ومن يضلل الله فما, باللغة نيانجا

﴿أليس الله بكاف عبده ويخوفونك بالذين من دونه ومن يضلل الله فما﴾ [الزُّمَر: 36]

Khaled Ibrahim Betala
“Kodi Allah sali Wokwanira kwa kapolo Wake? Koma akukuopseza ndi zina zosakhala Iye! Ndipo yemwe Allah wam’lekelera kuti asokere, ndithu alibe womuongola
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek