×

Mwina mzimu ungadzanene kuti, “Oh tsoka kwa ine chifukwa chakulephera kwanga pokwaniritsa 39:56 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Az-Zumar ⮕ (39:56) ayat 56 in Chichewa

39:56 Surah Az-Zumar ayat 56 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zumar ayat 56 - الزُّمَر - Page - Juz 24

﴿أَن تَقُولَ نَفۡسٞ يَٰحَسۡرَتَىٰ عَلَىٰ مَا فَرَّطتُ فِي جَنۢبِ ٱللَّهِ وَإِن كُنتُ لَمِنَ ٱلسَّٰخِرِينَ ﴾
[الزُّمَر: 56]

Mwina mzimu ungadzanene kuti, “Oh tsoka kwa ine chifukwa chakulephera kwanga pokwaniritsa udindo wanga kwa Mulungu! Ndithudi ine ndidali mmodzi wa iwo amene anali kunyoza.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: أن تقول نفس ياحسرتا على ما فرطت في جنب الله وإن كنت, باللغة نيانجا

﴿أن تقول نفس ياحسرتا على ما فرطت في جنب الله وإن كنت﴾ [الزُّمَر: 56]

Khaled Ibrahim Betala
“Kuti mzimu usadzanene: “Kalanga ine! Mzomwe sindidalabadire kumbali ya Allah; ndithu ndidali mmodzi wa ochitira chibwana (zinthu za chipembedzo).”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek