×

Kapena akhoza kunena kuti, “Akadakhala kuti Mulungu adanditsogolera, ndithudi, ine ndikadakhala m’gulu 39:57 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Az-Zumar ⮕ (39:57) ayat 57 in Chichewa

39:57 Surah Az-Zumar ayat 57 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zumar ayat 57 - الزُّمَر - Page - Juz 24

﴿أَوۡ تَقُولَ لَوۡ أَنَّ ٱللَّهَ هَدَىٰنِي لَكُنتُ مِنَ ٱلۡمُتَّقِينَ ﴾
[الزُّمَر: 57]

Kapena akhoza kunena kuti, “Akadakhala kuti Mulungu adanditsogolera, ndithudi, ine ndikadakhala m’gulu la anthu angwiro.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: أو تقول لو أن الله هداني لكنت من المتقين, باللغة نيانجا

﴿أو تقول لو أن الله هداني لكنت من المتقين﴾ [الزُّمَر: 57]

Khaled Ibrahim Betala
“Kapena ungadzanene: “Allah akadandiongola, ndithu ndikadakhala mwa oopa (Allah).”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek