×

Ndipo Mulungu adzapereka onse amene amalewa zoipa ku malo awo opambana. Palibe 39:61 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Az-Zumar ⮕ (39:61) ayat 61 in Chichewa

39:61 Surah Az-Zumar ayat 61 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zumar ayat 61 - الزُّمَر - Page - Juz 24

﴿وَيُنَجِّي ٱللَّهُ ٱلَّذِينَ ٱتَّقَوۡاْ بِمَفَازَتِهِمۡ لَا يَمَسُّهُمُ ٱلسُّوٓءُ وَلَا هُمۡ يَحۡزَنُونَ ﴾
[الزُّمَر: 61]

Ndipo Mulungu adzapereka onse amene amalewa zoipa ku malo awo opambana. Palibe choipa chimene chidzagwa pa iwo, ndipo iwo sadzamva chisoni ayi

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وينجي الله الذين اتقوا بمفازتهم لا يمسهم السوء ولا هم يحزنون, باللغة نيانجا

﴿وينجي الله الذين اتقوا بمفازتهم لا يمسهم السوء ولا هم يحزنون﴾ [الزُّمَر: 61]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo Allah adzawapulumutsa amene adamuopa, chifukwa cha kupambana kwawo. Zoipa sizikawakhudza, ndipo iwo sakadandaula
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek