×

Ndipo iwo sadamulemekeze Mulungu ndi ulemu umene uli woyenera kwa Iye ndipo 39:67 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Az-Zumar ⮕ (39:67) ayat 67 in Chichewa

39:67 Surah Az-Zumar ayat 67 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zumar ayat 67 - الزُّمَر - Page - Juz 24

﴿وَمَا قَدَرُواْ ٱللَّهَ حَقَّ قَدۡرِهِۦ وَٱلۡأَرۡضُ جَمِيعٗا قَبۡضَتُهُۥ يَوۡمَ ٱلۡقِيَٰمَةِ وَٱلسَّمَٰوَٰتُ مَطۡوِيَّٰتُۢ بِيَمِينِهِۦۚ سُبۡحَٰنَهُۥ وَتَعَٰلَىٰ عَمَّا يُشۡرِكُونَ ﴾
[الزُّمَر: 67]

Ndipo iwo sadamulemekeze Mulungu ndi ulemu umene uli woyenera kwa Iye ndipo dziko lapansi lidzakhala pa chikhato pake pa tsiku lachiweruzo. Kumwamba kudzakulungidwa m’dzanja lake lamanja. Ulemerero ukhale kwa Iye ndipo Iye ndi woposa mafano amene amamufanizira nawo

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وما قدروا الله حق قدره والأرض جميعا قبضته يوم القيامة والسموات مطويات, باللغة نيانجا

﴿وما قدروا الله حق قدره والأرض جميعا قبضته يوم القيامة والسموات مطويات﴾ [الزُّمَر: 67]

Khaled Ibrahim Betala
“Koma sadamlemekeze Allah, kulemekeza koyenerana Naye, pomwe pa tsiku la Qiyâma nthaka yonse (idzakhala) chofumbata Chake mmanja; ndipo thambo lidzakulungidwa ndi dzanja Lake lamanja. Walemekezeka Allah. Ndipo watukuka ku zimene akum’phatikiza nazozi
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek