×

Koma pamene mavuto akhazikika pa munthu, iye amapempha Ambuye wake pafupipafupi koma 39:8 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Az-Zumar ⮕ (39:8) ayat 8 in Chichewa

39:8 Surah Az-Zumar ayat 8 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zumar ayat 8 - الزُّمَر - Page - Juz 23

﴿۞ وَإِذَا مَسَّ ٱلۡإِنسَٰنَ ضُرّٞ دَعَا رَبَّهُۥ مُنِيبًا إِلَيۡهِ ثُمَّ إِذَا خَوَّلَهُۥ نِعۡمَةٗ مِّنۡهُ نَسِيَ مَا كَانَ يَدۡعُوٓاْ إِلَيۡهِ مِن قَبۡلُ وَجَعَلَ لِلَّهِ أَندَادٗا لِّيُضِلَّ عَن سَبِيلِهِۦۚ قُلۡ تَمَتَّعۡ بِكُفۡرِكَ قَلِيلًا إِنَّكَ مِنۡ أَصۡحَٰبِ ٱلنَّارِ ﴾
[الزُّمَر: 8]

Koma pamene mavuto akhazikika pa munthu, iye amapempha Ambuye wake pafupipafupi koma munthuyo akalandira chisomo chochokera kwa Ambuye wake iye amaiwala zimene amalilira poyamba ndipo amakhazikitsa opikisana ndi Mulungu ndi cholinga chosokoneza anthu ku njira yoyenera ya Mulungu. Nena “Basangalalani ndi kusakhulupirira kwanu kwa kanthawi kochepa. Ndithudi inu ndinu okakhala ku moto!”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإذا مس الإنسان ضر دعا ربه منيبا إليه ثم إذا خوله نعمة, باللغة نيانجا

﴿وإذا مس الإنسان ضر دعا ربه منيبا إليه ثم إذا خوله نعمة﴾ [الزُّمَر: 8]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo masautso akampeza munthu, amapempha Mbuye wake ndi kutembenukira kwa Iye (pomwe chikhalirecho adali kumnyoza). Kenako (Mbuye wake) akampatsa mtendere wochokera kwa Iye (waukulu), amaiwala (masautso aja) omwe adali kumpempha Allah kuti amchotsere asadampatse mtenderewo, ndipo kenako ndikumpangira Allah milungu inzake kuti asokeretse ku njira Yake. Nena (iwe Mtumiki kwa yemwe ali ndi chikhalidwe chotere): “Sangalala ndi kukanira kwako (mtendere wa Allah) kwa nthawi yochepa. Ndithu iwe ndi mmodzi wa anthu aku Moto.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek