×

oh inu anthu amene mudapatsidwa Buku! Khulupirirani zimene tavumbulutsa zimene zitsimikizira Maua 4:47 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:47) ayat 47 in Chichewa

4:47 Surah An-Nisa’ ayat 47 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 47 - النِّسَاء - Page - Juz 5

﴿يَٰٓأَيُّهَا ٱلَّذِينَ أُوتُواْ ٱلۡكِتَٰبَ ءَامِنُواْ بِمَا نَزَّلۡنَا مُصَدِّقٗا لِّمَا مَعَكُم مِّن قَبۡلِ أَن نَّطۡمِسَ وُجُوهٗا فَنَرُدَّهَا عَلَىٰٓ أَدۡبَارِهَآ أَوۡ نَلۡعَنَهُمۡ كَمَا لَعَنَّآ أَصۡحَٰبَ ٱلسَّبۡتِۚ وَكَانَ أَمۡرُ ٱللَّهِ مَفۡعُولًا ﴾
[النِّسَاء: 47]

oh inu anthu amene mudapatsidwa Buku! Khulupirirani zimene tavumbulutsa zimene zitsimikizira Maua Mulunguamenemulinawo, tisadatembenuzenkhope ndikuzibwezera kumbuyo kwake kapena kuwatemberera monga mmene tidawatemberera anthu ophwanya tsiku la Sabata. Ndipo lamulo la Mulungu limatsatidwa ndipo limakwaniritsidwa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ياأيها الذين أوتوا الكتاب آمنوا بما نـزلنا مصدقا لما معكم من قبل, باللغة نيانجا

﴿ياأيها الذين أوتوا الكتاب آمنوا بما نـزلنا مصدقا لما معكم من قبل﴾ [النِّسَاء: 47]

Khaled Ibrahim Betala
“E inu amene mwapatsidwa buku! Zikhulupirireni zomwe tavumbulutsa zikutsimikizira zomwe muli nazo tisanazisinthe nkhope zanu ndi kuzitembenuzira kumbuyo kwake, kapena tisanawatembelere monga momwe tidawatembelera omwe sadalemekeze kupatulika kwa tsiku la Sabata. Ndipo lamulo la Allah ndilochitikadi
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek