×

Ndithudi Mulungu sakhululukira kuti milungu izipembedzedwa yowonjezera pa Iye koma Iye amakhululukira 4:48 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:48) ayat 48 in Chichewa

4:48 Surah An-Nisa’ ayat 48 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 48 - النِّسَاء - Page - Juz 5

﴿إِنَّ ٱللَّهَ لَا يَغۡفِرُ أَن يُشۡرَكَ بِهِۦ وَيَغۡفِرُ مَا دُونَ ذَٰلِكَ لِمَن يَشَآءُۚ وَمَن يُشۡرِكۡ بِٱللَّهِ فَقَدِ ٱفۡتَرَىٰٓ إِثۡمًا عَظِيمًا ﴾
[النِّسَاء: 48]

Ndithudi Mulungu sakhululukira kuti milungu izipembedzedwa yowonjezera pa Iye koma Iye amakhululukira aliyense amene wamufuna pa machimo ena. Ndipo aliyense amene amapembedza milungu ina yowonjezera pa Iye, iye, ndithudi, wapeka bodza loopsya

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إن الله لا يغفر أن يشرك به ويغفر ما دون ذلك لمن, باللغة نيانجا

﴿إن الله لا يغفر أن يشرك به ويغفر ما دون ذلك لمن﴾ [النِّسَاء: 48]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithudi Allah sangakukhululuke kuphatikizidwa (ndi chinachake), koma amakhululuka (machimo ena) osati amenewa kwa amene wamfuna. Ndipo amene angamphatikize Allah, ndithudi, wadzipekera uchimo waukulu
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek