×

Pakati pa Ayuda pali ena amene amasinthitsa mawu m’malo mwake ndipo amati: 4:46 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:46) ayat 46 in Chichewa

4:46 Surah An-Nisa’ ayat 46 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 46 - النِّسَاء - Page - Juz 5

﴿مِّنَ ٱلَّذِينَ هَادُواْ يُحَرِّفُونَ ٱلۡكَلِمَ عَن مَّوَاضِعِهِۦ وَيَقُولُونَ سَمِعۡنَا وَعَصَيۡنَا وَٱسۡمَعۡ غَيۡرَ مُسۡمَعٖ وَرَٰعِنَا لَيَّۢا بِأَلۡسِنَتِهِمۡ وَطَعۡنٗا فِي ٱلدِّينِۚ وَلَوۡ أَنَّهُمۡ قَالُواْ سَمِعۡنَا وَأَطَعۡنَا وَٱسۡمَعۡ وَٱنظُرۡنَا لَكَانَ خَيۡرٗا لَّهُمۡ وَأَقۡوَمَ وَلَٰكِن لَّعَنَهُمُ ٱللَّهُ بِكُفۡرِهِمۡ فَلَا يُؤۡمِنُونَ إِلَّا قَلِيلٗا ﴾
[النِّسَاء: 46]

Pakati pa Ayuda pali ena amene amasinthitsa mawu m’malo mwake ndipo amati: “Ife tamva mau ako koma sitikumvera ndipo imva koma usamve chili chonse” ndipo amati: ‘Chenjera, timvere ife ndipo ife tidzakumvera’ ali kupotoza malirime awo ndi cholinga chotukwana chipembedzo. Koma iwo akadati: “Tamva ndipo tatsatira; tiphunzitse ife”; zikadawakhalira bwino kwambiri, koma Mulungu wawatemberera iwo chifukwa chosakhulupirira kwawo motero iwo sakhulupilira koma pang’ono

❮ Previous Next ❯

ترجمة: من الذين هادوا يحرفون الكلم عن مواضعه ويقولون سمعنا وعصينا واسمع غير, باللغة نيانجا

﴿من الذين هادوا يحرفون الكلم عن مواضعه ويقولون سمعنا وعصينا واسمع غير﴾ [النِّسَاء: 46]

❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek