Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 49 - النِّسَاء - Page - Juz 5
﴿أَلَمۡ تَرَ إِلَى ٱلَّذِينَ يُزَكُّونَ أَنفُسَهُمۚ بَلِ ٱللَّهُ يُزَكِّي مَن يَشَآءُ وَلَا يُظۡلَمُونَ فَتِيلًا ﴾
[النِّسَاء: 49]
﴿ألم تر إلى الذين يزكون أنفسهم بل الله يزكي من يشاء ولا﴾ [النِّسَاء: 49]
Khaled Ibrahim Betala “Kodi sukuwaona omwe akudziyeretsa okha? Koma Allah amamuyeretsa amene wamufuna (pomulimbikitsa kuchita zabwino). Ndipo sadzaponderezedwa ngakhale ndi kachinthu kochepa konga kaulusi kokhala mkati mwakhokho la tende |