×

Aliyense amene amathandiza kuchita ntchito zabwino adzalandira gawo lake la ntchitoyo, ndipo 4:85 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:85) ayat 85 in Chichewa

4:85 Surah An-Nisa’ ayat 85 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 85 - النِّسَاء - Page - Juz 5

﴿مَّن يَشۡفَعۡ شَفَٰعَةً حَسَنَةٗ يَكُن لَّهُۥ نَصِيبٞ مِّنۡهَاۖ وَمَن يَشۡفَعۡ شَفَٰعَةٗ سَيِّئَةٗ يَكُن لَّهُۥ كِفۡلٞ مِّنۡهَاۗ وَكَانَ ٱللَّهُ عَلَىٰ كُلِّ شَيۡءٖ مُّقِيتٗا ﴾
[النِّسَاء: 85]

Aliyense amene amathandiza kuchita ntchito zabwino adzalandira gawo lake la ntchitoyo, ndipo aliyense amene amathandiza kuchita ntchito zoipa naye adzakhala ndi gawo la uchimo. Ndipo Mulungu ali ndi mphamvu yochita chinthu china chilichonse

❮ Previous Next ❯

ترجمة: من يشفع شفاعة حسنة يكن له نصيب منها ومن يشفع شفاعة سيئة, باللغة نيانجا

﴿من يشفع شفاعة حسنة يكن له نصيب منها ومن يشفع شفاعة سيئة﴾ [النِّسَاء: 85]

Khaled Ibrahim Betala
“Amene angampemphere (mnzake) pempho labwino (lothandizira pa zabwino) adzapeza gawo mmenemo. Ndipo amene angampemphelere pemphero loipa, adzapeza gawo m’zoipazo. Ndipo Allah Ngodziwa chilichonse
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek