×

Kupatula okhawo amene gulu lina limene liri pakati panu ndipo inu mwachita 4:90 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nisa’ ⮕ (4:90) ayat 90 in Chichewa

4:90 Surah An-Nisa’ ayat 90 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nisa’ ayat 90 - النِّسَاء - Page - Juz 5

﴿إِلَّا ٱلَّذِينَ يَصِلُونَ إِلَىٰ قَوۡمِۭ بَيۡنَكُمۡ وَبَيۡنَهُم مِّيثَٰقٌ أَوۡ جَآءُوكُمۡ حَصِرَتۡ صُدُورُهُمۡ أَن يُقَٰتِلُوكُمۡ أَوۡ يُقَٰتِلُواْ قَوۡمَهُمۡۚ وَلَوۡ شَآءَ ٱللَّهُ لَسَلَّطَهُمۡ عَلَيۡكُمۡ فَلَقَٰتَلُوكُمۡۚ فَإِنِ ٱعۡتَزَلُوكُمۡ فَلَمۡ يُقَٰتِلُوكُمۡ وَأَلۡقَوۡاْ إِلَيۡكُمُ ٱلسَّلَمَ فَمَا جَعَلَ ٱللَّهُ لَكُمۡ عَلَيۡهِمۡ سَبِيلٗا ﴾
[النِّسَاء: 90]

Kupatula okhawo amene gulu lina limene liri pakati panu ndipo inu mwachita nawo pangano lokhazikitsa mtendere kapena adza kwa inu chifukwa mitima yawo yawaletsa kuti amenyane nanu kapena kumenyana ndi anthu a mtundu wawo. Mulungu akadafuna akadawapatsa iwo mphamvu zoti akugonjetseni inu, kotero akadamenyana nanu. Choncho ngati atalikirana nanu ndipo asiya kumenyana nanu ndi kukuonetsani mtendere, Mulungu wakulamulirani kuti musawaononge

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إلا الذين يصلون إلى قوم بينكم وبينهم ميثاق أو جاءوكم حصرت صدورهم, باللغة نيانجا

﴿إلا الذين يصلون إلى قوم بينكم وبينهم ميثاق أو جاءوكم حصرت صدورهم﴾ [النِّسَاء: 90]

Khaled Ibrahim Betala
“Kupatula omwe akugwirizana ndi anthu amene pali pangano pakati panu ndi iwo, kapena omwe akudza kwa inu uku zifuwa zawo zili zobanika kumenyana nanu, kapena kumenyana ndi anthu awo. (Oterewo musamenyane nawo). Ngati Allah akadafuna, akadawapatsa mphamvu yokugonjetserani, choncho akadakumenyani. Ngati atakupewani, osamenyana nanu ndipo nkukupatsani mtendere, ndiye kuti Allah sadakupangireni njira pa iwo (yakuti mumenyane nawo)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek