Quran with Chichewa translation - Surah Ghafir ayat 30 - غَافِر - Page - Juz 24
﴿وَقَالَ ٱلَّذِيٓ ءَامَنَ يَٰقَوۡمِ إِنِّيٓ أَخَافُ عَلَيۡكُم مِّثۡلَ يَوۡمِ ٱلۡأَحۡزَابِ ﴾
[غَافِر: 30]
﴿وقال الذي آمن ياقوم إني أخاف عليكم مثل يوم الأحزاب﴾ [غَافِر: 30]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo munthu wokhulupirira uja adanena: “E inu anthu anga! Ine ndikukuoperani (za tsiku la masautso) monga tsiku la magulu (omwe adaukira aneneri awo).” |