Quran with Chichewa translation - Surah Ghafir ayat 33 - غَافِر - Page - Juz 24
﴿يَوۡمَ تُوَلُّونَ مُدۡبِرِينَ مَا لَكُم مِّنَ ٱللَّهِ مِنۡ عَاصِمٖۗ وَمَن يُضۡلِلِ ٱللَّهُ فَمَا لَهُۥ مِنۡ هَادٖ ﴾
[غَافِر: 33]
﴿يوم تولون مدبرين ما لكم من الله من عاصم ومن يضلل الله﴾ [غَافِر: 33]
Khaled Ibrahim Betala ““Tsiku limene mudzathawa ndi kutembenuza misana yanu; pomwe simudzakhala ndi mtetezi ku chilango cha Allah; ndipo amene Allah wamulekelera kusokera (chifukwa cha zochita zake zoipa), ndiye kuti sangapeze muongoli.” |